Botanix – Buku la zomera

Botanix ya Chicheŵa

Archive of all articles

There you can find all articles which are available in this language section of Botanix.

Category: Zonse Bowa Malangizo a kalimidwe ka mbewu Mapalmu Tizilombo towononga mbewu Udzu Zomera za chilendo Zomera za m’madzi

Author:

2009

May (4)

Gawo: Zomera za chilendo

Malangizo a momwe tingalimire ndi kusamalira mbewu

Pongamia pinnata

chithunzi

Pongamia pinnata

Chinsense Pongamia pinnata (maina ena: Honge Tree, Pongam Tree, Panigrahi) ndi mtengo umene umapululuka masamba nyengo yozizira, pakati pa mamitala 15–25 kutalika, umene uli m’gulu la Fabaceae. Uli ndi m’mwamba mwamukulu ndi maluwa ang’onoang’ono ambiri oyera, pinki kapena violet. Unabadwa ku India, koma unafalikira kulimidwa ku m’mwera chakuvuma kwa Asia.

Lachinayi 24. November 2011 18:59 | purintani | Zomera za chilendo

Kudzala nthanga za mango

Mudzale nthanga za mango zongochotsedwa kumene kuti zimere bwino. Viyikani nthanga m’madzi ndi temperature yokwana 20–25°C kwa pafupifupi maola awiri mpaka asanu ndi imodzi.

Lachiwiri 22. November 2011 18:57 | purintani | Zomera za chilendo, Malangizo a kalimidwe ka mbewu

Mango a Kalimantan, Kasturi (Mangifera casturi)

Mango a Kalimantan (Mangifera casturi) kapena mu chilankhulo cha kuderako otchedwa Kasturi ndi mtengo wa zipatso opezeka kumadera otentha wautali 10–30 m umapezeka kawirikawiri kudera laling’ono lozungulira Banjarmasin ku Southern Borneo (Indonesia). Masiku ano supezekanso mchire chifukwa chakusavomerezekwa kodula zipika. Ngakhale zili chomwechi, ukulimidwabe m’derali chifukwa cha zipatso zake zokoma.

Lolemba 21. November 2011 18:55 | purintani | Zomera za chilendo

Fodya wa Mtengo Nicotiana glauca – Chomera chokongoletsa pamalo perspective!

chithunzi

Fodya wa Mtengo (Nicotiana glauca)

Khumbo la munthu ku chinthu chatsopano ndi chosachitikachitika lilibe malire. Alimi naonso amalota za chinthu chatsopano chimene angalime mmunda mwawo – chimene aliyense alibe. Msika wa mbewu nawonso umakhala ndi zinthu zatsopano za alimi – ndi cholinga choletsa njala imene alimi ofuna zinthu zabwino amakhala nayo. Kukhanzikitsidwa kwa malonda a mbewu zatsopano, kudzapangitsa kuti mitengo ya fodya izipezeka paliponse kwa alimi onse posachedwapa!

Loweruka 19. November 2011 18:31 | purintani | Zomera za chilendo

Ulimi wa Welwitschia mirabilis

chithunzi

Mbewu ya Welwitschia

Welwitschia (Welwitschia mirabilis) ndichomera chomwe chimamera ndi kukula m’kadera kakang’ono ka m‘mbali mwa nyanja ya mchere ya Atlantic mdziko la Namibia ndi kummwera kwa Angola. Welwitschia ndi mtengo weni-weni, ngakhale kuti sumaoneka choncho ukauona koyamba. Chomerachi chimakhala ndi chithime chimodzi chachifupi pomwe pamamela masamba awiri – omwe amaoneka ngati ma riboni awiri opiringizika. Welwitschia nthawi zina amaoneka ngati mulu wa zinyalala!

Lachisanu 18. November 2011 18:14 | purintani | Zomera za chilendo

Mbiri ya KPR

Chizindikiro cha KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera ku Slovakia
KPR - Bungwe la anthu osamalira zomera la KPR ndi bungwe lapadziko lonse lapansi. Werengani zambiri...
Gawani zomwe mukudziwa za kubyala mbewu komanso kusamalira zomera. Lembani nkhani zokhudza kubzyala ndi kusamalira mbewu komanso zomera, ndi zina zambiri, ndipo zisindikitseni muchinenero chanuchanu mu timabuku tathu ta Botanix! Lumikizanani nafe kuti mumve zambiri.

Category: Zonse Bowa Malangizo a kalimidwe ka mbewu Mapalmu Tizilombo towononga mbewu Udzu Zomera za chilendo Zomera za m’madzi