Kudzala mababu a maluwa ndi mmera
Chotsani mababu a maluwa ndi mmera amene mwalandira pa positi muphukusi, ndipo zisiyeni zikhale mumthunzi kwa masiku awiri kapena atatu. Chothekera chachiwiri ndikuzidzala nthawi yomweyo ndikuzisunga mumthunzi kwa masiku ochepa kuti zisafote ndi dzuwa.
Loweruka 26. November 2011 06:03 | purintani | Malangizo a kalimidwe ka mbewu
Kulima bowa wa mzikuni (Pleurotus ostreatus)
Bowa wa mzikuni (Pleurotus ostreatus) ndi wotchuka kuposa bowa wamba (champignon mushroom)! tsopano. Kutengera ndi bowa wamba, bowa wa mzikuni uli ndi ubwino umodzi waukulu – sungasokonezedwe ndi chinthu chokupha (Amanita phalloides).
Pongamia pinnata
Pongamia pinnata
Chinsense Pongamia pinnata (maina ena: Honge Tree, Pongam Tree, Panigrahi) ndi mtengo umene umapululuka masamba nyengo yozizira, pakati pa mamitala 15–25 kutalika, umene uli m’gulu la Fabaceae. Uli ndi m’mwamba mwamukulu ndi maluwa ang’onoang’ono ambiri oyera, pinki kapena violet. Unabadwa ku India, koma unafalikira kulimidwa ku m’mwera chakuvuma kwa Asia.
Lachinayi 24. November 2011 11:59 | purintani | Zomera za chilendo
Kalimidwe ka Four Leaf Clover (Marsilea quadrifolia)

The Four Leaf Clover (Marsilea quadrifolia) ndizomera mmadzi zimene masamba ake amaoneka ngati clover. Mukuganiza kuti pakati pa zomera zammadzi ndi clover palibe ubale? Mbali ina – zonse mwa zinthuzi zikukamba za chikhalidwe cha zomera zosapezekapezeka zokongola kwambiri mu ulimi.
Lachitatu 23. November 2011 11:58 | purintani | Malangizo a kalimidwe ka mbewu
Kudzala nthanga za mango
Mudzale nthanga za mango zongochotsedwa kumene kuti zimere bwino. Viyikani nthanga m’madzi ndi temperature yokwana 20–25°C kwa pafupifupi maola awiri mpaka asanu ndi imodzi.
Lachiwiri 22. November 2011 11:57 | purintani | Zomera za chilendo, Malangizo a kalimidwe ka mbewu
Mbiri ya KPR
Gawani zomwe mukudziwa za kubyala mbewu komanso kusamalira zomera. Lembani nkhani zokhudza kubzyala ndi kusamalira mbewu komanso zomera, ndi zina zambiri, ndipo zisindikitseni muchinenero chanuchanu mu timabuku tathu ta Botanix! Lumikizanani nafe kuti mumve zambiri.
Category: Zonse Bowa Malangizo a kalimidwe ka mbewu Mapalmu Tizilombo towononga mbewu Udzu Zomera za chilendo Zomera za m’madzi